2 Petulo 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Amalankhula mawu odzitukumula opanda pake. Ndipo amagwiritsa ntchito zilakolako za thupi+ komanso khalidwe lopanda manyazi* pokopa anthu amene angothawa kumene kwa anthu ochita zoipa.+
18 Amalankhula mawu odzitukumula opanda pake. Ndipo amagwiritsa ntchito zilakolako za thupi+ komanso khalidwe lopanda manyazi* pokopa anthu amene angothawa kumene kwa anthu ochita zoipa.+