Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 20:29, 30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ndikudziwa kuti ine ndikachoka, mimbulu yopondereza idzafika pakati panu+ ndipo sidzasamalira gulu la nkhosa mwachikondi. 30 Ndipo pakati panu anthu ena adzayamba kulankhula zinthu zopotoka kuti apatutse ophunzira aziwatsatira.+

  • 2 Petulo 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Komabe pakati pa Aisiraeli, anthu ena anakhala aneneri abodza.* Mofanana ndi zimenezi pakati panu padzakhalanso aphunzitsi abodza.*+ Anthu amenewa adzayambitsa mwachinsinsi timagulu towononga tampatuko ndipo adzakana ngakhale Ambuye wawo amene anawagula.+ Chifukwa chochita zimenezi, iwo adzawonongedwa mofulumira kwambiri.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena