-
2 Akorinto 9:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Chifukwa ndikudziwa kuti muli ndi mtima wofunitsitsa ndipo ndikunena zimenezi monyadira kwa anthu a ku Makedoniya. Ndikumawauza kuti abale a ku Akaya akhala okonzeka kwa chaka chimodzi tsopano, ndipo kudzipereka kwanu kwalimbikitsa abale ambiri kumeneko.
-