Mateyu 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mofanana ndi zimenezi, nanunso muzionetsa kuwala kwanu pamaso pa anthu,+ kuti aone ntchito zanu zabwino+ nʼkulemekeza Atate wanu wakumwamba.+ Chivumbulutso 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye ankanena mofuula kuti: “Opani Mulungu ndi kumupatsa ulemerero chifukwa ola lakuti apereke chiweruzo lafika.+ Choncho lambirani Iye amene anapanga kumwamba, dziko lapansi, nyanja+ ndi akasupe amadzi.”
16 Mofanana ndi zimenezi, nanunso muzionetsa kuwala kwanu pamaso pa anthu,+ kuti aone ntchito zanu zabwino+ nʼkulemekeza Atate wanu wakumwamba.+
7 Iye ankanena mofuula kuti: “Opani Mulungu ndi kumupatsa ulemerero chifukwa ola lakuti apereke chiweruzo lafika.+ Choncho lambirani Iye amene anapanga kumwamba, dziko lapansi, nyanja+ ndi akasupe amadzi.”