Mateyu 24:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako chizindikiro cha Mwana wa munthu chidzaonekera kumwamba ndipo mafuko onse apadziko lapansi adzadziguguda pachifuwa chifukwa cha chisoni.+ Iwo adzaona Mwana wa munthu+ akubwera pamitambo ya kumwamba ndi mphamvu ndiponso ulemerero waukulu.+
30 Kenako chizindikiro cha Mwana wa munthu chidzaonekera kumwamba ndipo mafuko onse apadziko lapansi adzadziguguda pachifuwa chifukwa cha chisoni.+ Iwo adzaona Mwana wa munthu+ akubwera pamitambo ya kumwamba ndi mphamvu ndiponso ulemerero waukulu.+