Salimo 47:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mulungu wakhala Mfumu ya mitundu ya anthu.+ Mulungu wakhala pampando wake wachifumu wopatulika. Yesaya 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chaka chimene Mfumu Uziya inamwalira,+ ine ndinaona Yehova atakhala pampando wachifumu wolemekezeka komanso wokwezeka,+ ndipo zovala zake zinadzaza mʼkachisi.
6 Chaka chimene Mfumu Uziya inamwalira,+ ine ndinaona Yehova atakhala pampando wachifumu wolemekezeka komanso wokwezeka,+ ndipo zovala zake zinadzaza mʼkachisi.