Salimo 141:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pemphero langa likhale ngati zofukiza+ zokonzedwa pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+ Chivumbulutso 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Utsi wa zofukizazo unakwera pamaso pa Mulungu kuchokera mʼdzanja la mngeloyo limodzi ndi mapemphero+ a oyera.
2 Pemphero langa likhale ngati zofukiza+ zokonzedwa pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+
4 Utsi wa zofukizazo unakwera pamaso pa Mulungu kuchokera mʼdzanja la mngeloyo limodzi ndi mapemphero+ a oyera.