Yohane 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndine mʼbusa wabwino.+ Mʼbusa wabwino amapereka moyo wake chifukwa cha nkhosa.+