Chivumbulutso 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndinaona Mwanawankhosa+ akumatula chidindo chimodzi mwa zidindo 7 zija,+ ndipo ndinamva mngelo mmodzi mwa angelo 4 aja+ akulankhula ndi mawu omveka ngati kugunda kwa bingu kuti: “Bwera!”
6 Ndinaona Mwanawankhosa+ akumatula chidindo chimodzi mwa zidindo 7 zija,+ ndipo ndinamva mngelo mmodzi mwa angelo 4 aja+ akulankhula ndi mawu omveka ngati kugunda kwa bingu kuti: “Bwera!”