Chivumbulutso 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Filadefiya lemba kuti: Izi ndi zimene akunena woyerayo,+ amene ndi woona,+ yemwe ali ndi kiyi wa Davide.+ Iye amene amati akatsegula palibe amene angatseke, ndipo akatseka palibe amene angatsegule.
7 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Filadefiya lemba kuti: Izi ndi zimene akunena woyerayo,+ amene ndi woona,+ yemwe ali ndi kiyi wa Davide.+ Iye amene amati akatsegula palibe amene angatseke, ndipo akatseka palibe amene angatsegule.