Machitidwe 26:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Zoti Khristu adzavutika,+ ndipo monga woyamba kuukitsidwa,+ adzalalikira kwa anthu awa ndiponso kwa anthu a mitundu ina zokhudza kuwala.”+ Akolose 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye ndi mutu wa thupi, lomwe ndi mpingo.+ Iye ndi chiyambi, woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa,+ kuti adzakhale woyamba pa zinthu zonse. Chivumbulutso 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso kuchokera kwa Yesu Khristu, “Mboni Yokhulupirika,”+ “woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa”+ ndiponso “Wolamulira mafumu a dziko lapansi.”+ Kwa iye amene amatikonda+ komanso amene anatimasula ku machimo athu pogwiritsa ntchito magazi ake,+
23 Zoti Khristu adzavutika,+ ndipo monga woyamba kuukitsidwa,+ adzalalikira kwa anthu awa ndiponso kwa anthu a mitundu ina zokhudza kuwala.”+
18 Iye ndi mutu wa thupi, lomwe ndi mpingo.+ Iye ndi chiyambi, woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa,+ kuti adzakhale woyamba pa zinthu zonse.
5 Komanso kuchokera kwa Yesu Khristu, “Mboni Yokhulupirika,”+ “woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa”+ ndiponso “Wolamulira mafumu a dziko lapansi.”+ Kwa iye amene amatikonda+ komanso amene anatimasula ku machimo athu pogwiritsa ntchito magazi ake,+