Chivumbulutso 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kuzungulira mpando wachifumuwo panalinso mipando yachifumu yokwana 24. Pamipando yachifumuyo, ndinaona patakhala akulu 24+ atavala zovala zoyera komanso zisoti zachifumu zagolide kumutu kwawo. Chivumbulutso 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiye akulu 24+ ndi angelo 4 aja,+ anagwada pansi nʼkuwerama ndipo analambira Mulungu amene wakhala pampando wachifumu, nʼkunena kuti: “Ame! Tamandani Ya!”*+
4 Kuzungulira mpando wachifumuwo panalinso mipando yachifumu yokwana 24. Pamipando yachifumuyo, ndinaona patakhala akulu 24+ atavala zovala zoyera komanso zisoti zachifumu zagolide kumutu kwawo.
4 Ndiye akulu 24+ ndi angelo 4 aja,+ anagwada pansi nʼkuwerama ndipo analambira Mulungu amene wakhala pampando wachifumu, nʼkunena kuti: “Ame! Tamandani Ya!”*+