Yakobo 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mwakufuna kwake, iye anatibereka pamene tinakhulupirira mawu ake omwe ndi choonadi.+ Anachita zimenezi kuti tikhale zipatso zoyambirira pa zolengedwa zake.+
18 Mwakufuna kwake, iye anatibereka pamene tinakhulupirira mawu ake omwe ndi choonadi.+ Anachita zimenezi kuti tikhale zipatso zoyambirira pa zolengedwa zake.+