Yoweli 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yambani kumweta ndi chikwakwa, chifukwa zokolola zacha. Bwerani nʼkuyamba kuponda chifukwa moponderamo mphesa mwadzaza.+ Malo ogweramo vinyo asefukira, chifukwa zoipa zawo zachuluka kwambiri.
13 Yambani kumweta ndi chikwakwa, chifukwa zokolola zacha. Bwerani nʼkuyamba kuponda chifukwa moponderamo mphesa mwadzaza.+ Malo ogweramo vinyo asefukira, chifukwa zoipa zawo zachuluka kwambiri.