Mateyu 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho inenso ndikukuuza kuti: Iwe ndiwe Petulo+ ndipo pathanthwe+ ili ndidzamangapo mpingo wanga. Mageti a Manda* sadzaugonjetsa. Yohane 6:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Aliyense amene amadya mnofu wanga ndi kumwa magazi anga adzapeza moyo wosatha, ndipo ndidzamuukitsa+ pa tsiku lomaliza. Yohane 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yesu anamuuza kuti: “Ine ndine kuuka ndi moyo.+ Aliyense wokhulupirira ine, ngakhale atamwalira, adzakhalanso ndi moyo.
18 Choncho inenso ndikukuuza kuti: Iwe ndiwe Petulo+ ndipo pathanthwe+ ili ndidzamangapo mpingo wanga. Mageti a Manda* sadzaugonjetsa.
54 Aliyense amene amadya mnofu wanga ndi kumwa magazi anga adzapeza moyo wosatha, ndipo ndidzamuukitsa+ pa tsiku lomaliza.
25 Yesu anamuuza kuti: “Ine ndine kuuka ndi moyo.+ Aliyense wokhulupirira ine, ngakhale atamwalira, adzakhalanso ndi moyo.