Chivumbulutso 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chilombocho chinakakamiza anthu onse, olemekezeka ndi onyozeka, olemera ndi osauka, mfulu ndi akapolo, kuti aikidwe chizindikiro padzanja lawo lamanja kapena pachipumi pawo.+ Chivumbulutso 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Apa mʼpamene pakufunika nzeru: Amene ali ndi nzeru awerengere nambala ya chilombocho, chifukwa ndi nambala ya munthu. Nambala yake ndi 666.+
16 Chilombocho chinakakamiza anthu onse, olemekezeka ndi onyozeka, olemera ndi osauka, mfulu ndi akapolo, kuti aikidwe chizindikiro padzanja lawo lamanja kapena pachipumi pawo.+
18 Apa mʼpamene pakufunika nzeru: Amene ali ndi nzeru awerengere nambala ya chilombocho, chifukwa ndi nambala ya munthu. Nambala yake ndi 666.+