Chivumbulutso 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mngelo wachiwiri analiza lipenga lake. Ndipo chinachake chokhala ngati phiri lalikulu limene likuyaka moto chinaponyedwa mʼnyanja.+ Zitatero gawo limodzi mwa magawo atatu a nyanja, linasanduka magazi.+
8 Mngelo wachiwiri analiza lipenga lake. Ndipo chinachake chokhala ngati phiri lalikulu limene likuyaka moto chinaponyedwa mʼnyanja.+ Zitatero gawo limodzi mwa magawo atatu a nyanja, linasanduka magazi.+