Chivumbulutso 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mngelo wachitatu analiza lipenga lake. Ndipo nyenyezi yaikulu imene inkayaka ngati nyale inagwa kuchokera kumwamba. Inagwera pagawo limodzi mwa magawo atatu a mitsinje, ndi pa akasupe a madzi.+
10 Mngelo wachitatu analiza lipenga lake. Ndipo nyenyezi yaikulu imene inkayaka ngati nyale inagwa kuchokera kumwamba. Inagwera pagawo limodzi mwa magawo atatu a mitsinje, ndi pa akasupe a madzi.+