Ekisodo 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nthawi yomweyo Mose ndi Aroni anachita mogwirizana ndi zimene Yehova anawalamula. Aroni anatenga ndodo yake nʼkumenya madzi amumtsinje wa Nailo, Farao ndi atumiki ake akuona ndipo madzi onse amumtsinje wa Nailo anasanduka magazi.+ Salimo 78:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Sanakumbukirenso mmene anasandutsira madzi amʼngalande zotuluka mumtsinje wa Nailo kukhala magazi,+Moti sanathe kumwa madziwo.
20 Nthawi yomweyo Mose ndi Aroni anachita mogwirizana ndi zimene Yehova anawalamula. Aroni anatenga ndodo yake nʼkumenya madzi amumtsinje wa Nailo, Farao ndi atumiki ake akuona ndipo madzi onse amumtsinje wa Nailo anasanduka magazi.+
44 Sanakumbukirenso mmene anasandutsira madzi amʼngalande zotuluka mumtsinje wa Nailo kukhala magazi,+Moti sanathe kumwa madziwo.