Salimo 145:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova ndi wolungama mʼnjira zake zonse,+Ndipo ndi wokhulupirika pa chilichonse chimene amachita.+ Chivumbulutso 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Popeza inu nokha Yehova* ndinu wokhulupirika, ndi ndani amene sadzakuopani komanso kulemekeza dzina lanu?+ Anthu a mitundu yonse adzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa iwo adziwa malamulo anu olungama.”
17 Yehova ndi wolungama mʼnjira zake zonse,+Ndipo ndi wokhulupirika pa chilichonse chimene amachita.+
4 Popeza inu nokha Yehova* ndinu wokhulupirika, ndi ndani amene sadzakuopani komanso kulemekeza dzina lanu?+ Anthu a mitundu yonse adzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa iwo adziwa malamulo anu olungama.”