Chivumbulutso 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma za chinsinsi chopatulika cha nyenyezi 7 zimene waona mʼdzanja langa lamanja ndiponso za chinsinsi cha zoikapo nyale 7 zagolide, tanthauzo lake ndi ili: Nyenyezi 7 zikuimira angelo a mipingo 7, ndipo zoikapo nyale 7 zikuimira mipingo 7.”+
20 Koma za chinsinsi chopatulika cha nyenyezi 7 zimene waona mʼdzanja langa lamanja ndiponso za chinsinsi cha zoikapo nyale 7 zagolide, tanthauzo lake ndi ili: Nyenyezi 7 zikuimira angelo a mipingo 7, ndipo zoikapo nyale 7 zikuimira mipingo 7.”+