-
Ekisodo 10:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula dzanja lako ndi kuloza kumwamba kuti mʼdziko lonse la Iguputo mugwe mdima wandiweyani.”
-
-
Yesaya 8:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Kenako adzayangʼana padziko lapansi ndipo adzangoonapo kuzunzika, mdima, kusowa mtengo wogwira, nthawi zovuta, mdima wandiweyani ndipo sadzaonapo kuwala.
-