Machitidwe 20:29, 30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndikudziwa kuti ine ndikachoka, mimbulu yopondereza idzafika pakati panu+ ndipo sidzasamalira gulu la nkhosa mwachikondi. 30 Ndipo pakati panu anthu ena adzayamba kulankhula zinthu zopotoka kuti apatutse ophunzira aziwatsatira.+ 2 Akorinto 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu amenewa ndi atumwi onama, antchito achinyengo ndipo amadzichititsa kuoneka ngati atumwi a Khristu.+ 1 Yohane 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Abale okondedwa, musamakhulupirire mawu alionse ouziridwa,*+ koma muzifufuza mawu ouziridwawo* kuti muone ngati alidi ochokera kwa Mulungu,+ chifukwa aneneri abodza* ambiri ayamba kupezeka mʼdzikoli.+
29 Ndikudziwa kuti ine ndikachoka, mimbulu yopondereza idzafika pakati panu+ ndipo sidzasamalira gulu la nkhosa mwachikondi. 30 Ndipo pakati panu anthu ena adzayamba kulankhula zinthu zopotoka kuti apatutse ophunzira aziwatsatira.+
13 Anthu amenewa ndi atumwi onama, antchito achinyengo ndipo amadzichititsa kuoneka ngati atumwi a Khristu.+
4 Abale okondedwa, musamakhulupirire mawu alionse ouziridwa,*+ koma muzifufuza mawu ouziridwawo* kuti muone ngati alidi ochokera kwa Mulungu,+ chifukwa aneneri abodza* ambiri ayamba kupezeka mʼdzikoli.+