Chivumbulutso 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Onse amene ndimawakonda, ndimawadzudzula komanso kuwalanga.+ Choncho khala wodzipereka ndipo ulape.+
19 Onse amene ndimawakonda, ndimawadzudzula komanso kuwalanga.+ Choncho khala wodzipereka ndipo ulape.+