Chivumbulutso 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho ulape. Ngati sulapa, ndibwera kwa iwe mwamsanga, ndipo ndidzamenyana nawo ndi lupanga lalitali lamʼkamwa mwanga.+
16 Choncho ulape. Ngati sulapa, ndibwera kwa iwe mwamsanga, ndipo ndidzamenyana nawo ndi lupanga lalitali lamʼkamwa mwanga.+