Yohane 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Mawu ameneyo anakhala ndi thupi la nyama+ ndipo ankakhala pakati pathu. Ife tinaona ulemerero wake, ulemerero wofanana ndi umene mwana wobadwa yekha+ amalandira kuchokera kwa bambo ake. Mulungu ankamukomera mtima kwambiri* komanso ankaphunzitsa choonadi. Chivumbulutso 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Laodikaya,+ lemba kuti: Izi ndi zimene Ame+ akunena, yemwe ndi mboni+ yokhulupirika komanso yoona,+ woyamba wa chilengedwe cha Mulungu.+
14 Choncho Mawu ameneyo anakhala ndi thupi la nyama+ ndipo ankakhala pakati pathu. Ife tinaona ulemerero wake, ulemerero wofanana ndi umene mwana wobadwa yekha+ amalandira kuchokera kwa bambo ake. Mulungu ankamukomera mtima kwambiri* komanso ankaphunzitsa choonadi.
14 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Laodikaya,+ lemba kuti: Izi ndi zimene Ame+ akunena, yemwe ndi mboni+ yokhulupirika komanso yoona,+ woyamba wa chilengedwe cha Mulungu.+