-
Ezekieli 39:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Koma iwe mwana wa munthu, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Uza mbalame zamtundu uliwonse ndi zilombo zonse zakutchire kuti, “Sonkhanani pamodzi ndipo mubwere kuno. Zungulirani nsembe yanga imene ndikukukonzerani. Imeneyi ndi nsembe yaikulu mʼmapiri a ku Isiraeli.+ Mukabwera mudzadya nyama ndi kumwa magazi.+
-