Chivumbulutso 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako ndinaona mauthenga atatu onyansa ouziridwa,* amene ankaoneka ngati achule. Mauthengawo ankatuluka mʼkamwa mwa chinjoka,+ mʼkamwa mwa chilombo ndi mʼkamwa mwa mneneri wabodza.
13 Kenako ndinaona mauthenga atatu onyansa ouziridwa,* amene ankaoneka ngati achule. Mauthengawo ankatuluka mʼkamwa mwa chinjoka,+ mʼkamwa mwa chilombo ndi mʼkamwa mwa mneneri wabodza.