Chivumbulutso 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo chinaloledwa kupereka mpweya* kwa chifaniziro cha chilombo chija, kuti chifaniziro cha chilombocho chithe kulankhula komanso kuchititsa kuti onse amene akukana kulambira chifaniziro cha chilombocho aphedwe.
15 Ndipo chinaloledwa kupereka mpweya* kwa chifaniziro cha chilombo chija, kuti chifaniziro cha chilombocho chithe kulankhula komanso kuchititsa kuti onse amene akukana kulambira chifaniziro cha chilombocho aphedwe.