Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 10:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Musachite mantha ndi amene amapha thupi koma sangathe kupha moyo.+ Mʼmalomwake, muziopa amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe mʼGehena.*+

  • 2 Petulo 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Anawononganso mizinda ya Sodomu ndi Gomora poitentha ndi moto.+ Anachita zimenezi kuti likhale chenjezo kwa anthu osaopa Mulungu la zimene zidzawachitikire mʼtsogolo.+

  • Yuda 7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mofanana ndi zimenezi, anthu amʼmizinda ya Sodomu ndi Gomora komanso mizinda yozungulira ankachita chiwerewere* chonyansa kwambiri ndiponso kugonana mʼnjira imene si yachibadwa.+ Anthu amenewa anapatsidwa chilango cha chiwonongeko chosatha*+ ndipo ndi chitsanzo chotichenjeza.

  • Chivumbulutso 20:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndipo imfa ndi Manda* zinaponyedwa mʼnyanja yamoto.+ Nyanja yamoto+ imeneyi ikuimira imfa yachiwiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena