Chivumbulutso 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho ulape. Ngati sulapa, ndibwera kwa iwe mwamsanga, ndipo ndidzamenyana nawo ndi lupanga lalitali lamʼkamwa mwanga.+ Chivumbulutso 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nditayangʼana, ndinaona hatchi yoyera+ ndipo amene anakwera pahatchiyi ananyamula uta. Iye anapatsidwa chisoti chachifumu+ nʼkupita kukagonjetsa adani ake ndipo anapambana pankhondo yolimbana nawo.+
16 Choncho ulape. Ngati sulapa, ndibwera kwa iwe mwamsanga, ndipo ndidzamenyana nawo ndi lupanga lalitali lamʼkamwa mwanga.+
2 Nditayangʼana, ndinaona hatchi yoyera+ ndipo amene anakwera pahatchiyi ananyamula uta. Iye anapatsidwa chisoti chachifumu+ nʼkupita kukagonjetsa adani ake ndipo anapambana pankhondo yolimbana nawo.+