-
Chivumbulutso 4:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Kenako nthawi yomweyo mzimu wa Mulungu unayamba kugwira ntchito mwa ine ndipo mpando wachifumu unaoneka uli pamalo ake kumwamba, wina atakhalapo.+ 3 Amene anakhala pampandoyo ankaoneka ngati mwala wa yasipi+ komanso mwala wa sadiyo.* Utawaleza wooneka ngati mwala wa emarodi unazungulira mpando wachifumuwo.+
-