Yesaya 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye adzameza* imfa kwamuyaya+Ndipo Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzapukuta misozi pankhope zonse za anthu.+ Adzachotsa kunyozeka kwa anthu ake padziko lonse lapansi,Chifukwa Yehova ndi amene wanena zimenezi. 1 Akorinto 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Imfa nayonso, yomwe ndi mdani womaliza, idzawonongedwa.+
8 Iye adzameza* imfa kwamuyaya+Ndipo Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzapukuta misozi pankhope zonse za anthu.+ Adzachotsa kunyozeka kwa anthu ake padziko lonse lapansi,Chifukwa Yehova ndi amene wanena zimenezi.