Chivumbulutso 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kumpando wachifumuko kunkatuluka mphezi,+ mawu komanso mabingu.+ Panalinso nyale zamoto 7 zimene zinkayaka patsogolo pa mpando wachifumuwo. Nyalezo zikuimira mizimu 7 ya Mulungu.+
5 Kumpando wachifumuko kunkatuluka mphezi,+ mawu komanso mabingu.+ Panalinso nyale zamoto 7 zimene zinkayaka patsogolo pa mpando wachifumuwo. Nyalezo zikuimira mizimu 7 ya Mulungu.+