Mateyu 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musachite mantha ndi amene amapha thupi koma sangathe kupha moyo.+ Mʼmalomwake, muziopa amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe mʼGehena.*+
28 Musachite mantha ndi amene amapha thupi koma sangathe kupha moyo.+ Mʼmalomwake, muziopa amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe mʼGehena.*+