-
Ezekieli 47:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Kumbali zonse zamʼmphepete mwa mtsinjewo mudzamera mitengo yosiyanasiyana ya zipatso. Masamba ake sadzafota ndipo zipatso zake sizidzatha. Mwezi uliwonse mitengoyo izidzabereka zipatso chifukwa chakuti madzi ake akuchokera kumalo opatulika.+ Zipatso zake zidzakhala chakudya ndipo masamba ake adzakhala mankhwala.”+
-