Yohane 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngati zimenezi mukuzidziwa, mudzakhala osangalala mukamazichita.+ Chivumbulutso 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Wosangalala ndi munthu amene amawerenga mokweza komanso anthu amene akumva mawu a ulosi umenewu, ndiponso amene akutsatira zimene zalembedwa mmenemo,+ chifukwa nthawi yoikidwiratu yayandikira.
3 Wosangalala ndi munthu amene amawerenga mokweza komanso anthu amene akumva mawu a ulosi umenewu, ndiponso amene akutsatira zimene zalembedwa mmenemo,+ chifukwa nthawi yoikidwiratu yayandikira.