Salimo 62:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komanso chikondi chokhulupirika ndi chanu, inu Yehova,+Chifukwa inu mumabwezera aliyense mogwirizana ndi zochita zake.+ Yesaya 40:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Taonani! Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzabwera nʼkuonetsa mphamvu zake,Ndipo dzanja* lake lizidzalamulira mʼmalo mwa iyeyo.+ Mphoto yake ili ndi iyeyo,Ndipo malipiro amene amapereka ali pamaso pake.+ Aroma 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzaweruza aliyense mogwirizana ndi zochita zake.+
12 Komanso chikondi chokhulupirika ndi chanu, inu Yehova,+Chifukwa inu mumabwezera aliyense mogwirizana ndi zochita zake.+
10 Taonani! Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzabwera nʼkuonetsa mphamvu zake,Ndipo dzanja* lake lizidzalamulira mʼmalo mwa iyeyo.+ Mphoto yake ili ndi iyeyo,Ndipo malipiro amene amapereka ali pamaso pake.+