Yohane 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma amene adzamwe madzi amene ine ndidzamupatse sadzamvanso ludzu ngakhale pangʼono.+ Madzi amene ndidzamupatsewo adzasanduka kasupe wa madzi amene akutuluka mwa iye nʼkumupatsa moyo wosatha.”+
14 Koma amene adzamwe madzi amene ine ndidzamupatse sadzamvanso ludzu ngakhale pangʼono.+ Madzi amene ndidzamupatsewo adzasanduka kasupe wa madzi amene akutuluka mwa iye nʼkumupatsa moyo wosatha.”+