Chivumbulutso 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndinaona chizindikiro china kumwamba, chachikulu ndi chodabwitsa. Chizindikiro chimenechi chinali angelo 7+ amene anali ndi miliriĀ 7. Miliri imeneyi ndi yomaliza chifukwa ikamatha, mkwiyo wa Mulungu udzakhalanso utatha.+
15 Ndinaona chizindikiro china kumwamba, chachikulu ndi chodabwitsa. Chizindikiro chimenechi chinali angelo 7+ amene anali ndi miliriĀ 7. Miliri imeneyi ndi yomaliza chifukwa ikamatha, mkwiyo wa Mulungu udzakhalanso utatha.+