-
2 Akorinto 7:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndipo taonani mmene chisoni chogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu chimenechi chakuthandizirani. Chakuthandizani kukhala akhama kwambiri, chakuchititsani kudziyeretsa, kuipidwa ndi choipa, kukhala ndi mantha, kufunitsitsa kulapa, kukhala odzipereka ndiponso kukonza zolakwika.+ Mwasonyeza kuti ndinu oyera* mʼmbali zonse pa nkhani imeneyi.
-