Tsiku la Yehova komanso gulu lalikulu la asilikali ake (1-11)
Anawauza kuti abwerere kwa Yehova (12-17)
Yehova anayankha anthu ake (18-32)
“Ndidzapereka mzimu wanga” (28)
Zodabwitsa kumwamba ndi padziko lapansi (30)
Oitana pa dzina la Yehova adzapulumuka (32)