Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zimene Zili M‘buku la Habakuku HABAKUKU ZIMENE ZILI MʼBUKULI 1 Mneneri anapempha thandizo (1-4) ‘Inu Yehova, mpaka liti?’ (2) “Nʼchifukwa chiyani mukulekerera kuponderezana?” (3) Mulungu anagwiritsa ntchito Akasidi popereka chiweruzo (5-11) Mneneri anachonderera Yehova (12-17) ‘Inu Mulungu wanga, simufa’ (12) ‘Ndinu woyera moti simungaonerere zinthu zoipa’ (13) 2 ‘Ndidzakhala tcheru kuti ndione zimene adzanene’ (1) Zimene Yehova anayankha mneneri (2-20) ‘Uziyembekezerabe masomphenyawo’ (3) Wolungama adzakhala ndi moyo chifukwa cha kukhulupirika (4) Masoka 5 a Akasidi (6-20) Anthu odziwa Yehova adzadzaza dziko lapansi (14) 3 Mneneri anapemphera kwa Yehova kuti achitepo kanthu (1-19) Mulungu adzapulumutsa anthu ake odzozedwa (13) Kusangalala chifukwa cha Yehova ngakhale pali mavuto (17, 18)