Posinthira—1914
Olemba mbiri amanena kuti 1914 inali posinthira m’mbiri. Komabe Baibulo kalekale linali litaneneratu kuti ikakhala. Kodi nchiyani chimene Baibulo limanena ponena za 1914? Kodi ndimotani mmene inu mwayambukiridwira ndi zomwe zinachitika panthawiyo?
Mayankho okhutiritsa aperekedwa m’bukhu lakuti True Peace and Security—How Can You Find It? Wonani mutu wakuti “Chaka Chosonyezedwa—1914 C.E.” Kuchiyambiyambi kwa tsamba 70. Bukhu limeneli, lomwe lapendedwanso posachedwapa, mozizwitsa lafikira pogawiridwa mofala kwambiri kufikira kumakope mamiliyoni 33 m’zinenero 66. Pezani kope lanu. $1,40 zokha.
Chonde, tumizani mutalipiriratu positi, bukhu lachikuto cholimba, lamasamba 192 lakuti True Peace and Security—How Can You Find It? Ndatumiza $1,40 (Choperekacho chingathe kusintha).