Tsamba 2
“Timadziŵa mmene tingapezere miyala ya mtengo wapatali mu zikamba za nsomba zotchedwa oysters, golidi kuchokera mu mapiri ndi malasha kuchokera kunsi kwa dziko lapansi, koma sitidziŵa chirichonse ponena za magwero auzimu, chizimezime chopanga, chimene mwana amabisa mkati mwa iyemwini pamene alowa m’dziko lino.”—Dr. Maria Montessori