Tumizani Kulembetsa kwa Mphatso
Kali kachitidwe kachikondi kupereka chidziŵitso chofunika kwambiri ku ubwino wa winawake. Mamiliyoni ochulukira akulandira mokhazikika chidziŵitso choterocho kuchokera mu Nsanja ya Olonda ndi Galamukani!
Gawanani ndi mabwenzi anu. Tumizani mphatso ya kulembetsa kwa iwo mwa kutitumizira pepala limodzi kapena ochulukira omwe ali pansipa, mukumatsekeramo K48 limodzi ndi kapepala kamodzi.
Chonde tumizani kulembetsa kwa mphatso kwa chaka chimodzi kaamba ka Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! kwa munthu wotsatirayu, limodzinso ndi kalata yolongosola kuti iri mphatso yochokera kwa ________ (dzina lanu). Ndatsekeramo K48 (Zambia).