Yesani Mosamalitsa Mafunso Awa
✔ KODI INU MUFUNIKIRA KUTAYA KULEMERA?
✔ KODI MUKUFUNA KUKUTAYA IKO?
✔ KODI INU MUDZAPEŴA ZAKUDYA ZOKOMA KUDYA KOMA ZOSAPATSA THANZI?
✔ KODI INU MUDZAŴERENGA MACALORIE?
✔ KODI INU MUDZASEŴERA MOKHAZIKIKA?
✔ KODI METABOLISM YANU IDZATHANDIZA?
✔ KODI MUDZAPATSA MLANDU MAGLAND ANU?
✔ KODI MASELO A MAFUTA ANU ALI AAKULU KWAMBIRI?
✔ KODI ALI AMBIRI KOPOSA?
✔ KODI MAGENE ANU ALI MUMKHALIDWE WOIPA?
✔ KODI CHONULIRAPO CHANU CHIRI CHENICHENI?
✔ KODI KULEMERA KOTAYIDWA KUDZAKHALABE KOTAYIDWA?
MZERA WA KUNSI: KODI IRI YOLIMBA CHOTANI MPHAMVU YANU YA CHIFUNO NDI YA KUKHALABE?