Mamiliyoni Omwe Ali ndi Moyo Tsopano Sadzafa Konse
Uku sikuli kunena kopeka. Pali zifukwa zomvekera bwino za kukhulupirira icho.
Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! mokhazikika amalozera ku zifukwa zozikidwa pa Baibulo zimenezi. Tumizani kokha K75 ndipo mudzalandira magazini onse aŵiri (makope atatu pa mwezi) kaamba ka chaka chimodzi, titalipiriratu positi.