Zamkatimu
March 8, 2000
Ukapolo Wamakono—Uli Pafupi Kutha!
Anthu miyandamiyanda, makamaka amayi ndi ana, akukhala monga akapolo enieni. Kodi ukapolo umenewu udzatha bwanji?
5 Kodi Ndani Ali Akapolo Lerolino?
9 Ukapolo Wamakono Uli Pafupi Kutha!
15 Tinapatsidwa Chikhumbo Chokhala ndi Moyo
18 Chiyembekezo Chotsimikizika
32 “Ndiyenera Kudalira Mulungu”
Anthu a ku Russia Akuyamikira Ufulu wa Kulambira 22
Kuyambira mu 1991, anthu okhala m’dziko lomwe kale linkatchedwa Soviet Union akhala ndi ufulu waukulupo wa kulambira Mulungu. Anthu amene anachoka m’dzikolo kukakhala m’mayiko ena ayamikiranso ufulu wotere.
N’chifukwa Chiyani Bwenzi Langa Linandikhumudwitsa? 29
Nthaŵi zina ubwenzi umasokonezeka. Kodi zimenezi zimachitika bwanji? Kodi mungachitepo Chiyani Pankhaniyi?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
CHIKUTO: Kuzungulira kuyambira pamwamba chakumanja: CHITHUNZI CHA UN 148000/Jean Pierre Laffont; UNITED NATIONS/ J.P. LAFFONT; J.R. Ripper/RF2; J.R. Ripper/RF2; CHITHUNZI CHA UN 152227 chojambulidwa ndi John Isaac; pakati: Chithunzi cha United Nations: 151730
UNITED NATIONS/J.P. LAFFONT