Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 6/08 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2008
  • Nkhani Yofanana
  • Zidole Zina Si Zongoseweretsa
    Galamukani!—2008
  • Zoseŵeretsa Ana Zabwino Kwambiri
    Galamukani!—2004
  • Kodi Akambuku Akuluakulu a ku Siberia Satheratu?
    Galamukani!—2008
  • Kulankhulana ndi Achinyamata
    Nsanja ya Olonda—2008
Onani Zambiri
Galamukani!—2008
g 6/08 tsamba 1-2

Zamkatimu

June 2008

Kodi Ana Anu Mumawadziwa Bwino?

Ana ambiri amasintha makhalidwe ndiponso maonekedwe awo mwamsanga. Kodi makolo angawathandize bwanji pa nkhani imeneyi? Nanga kodi Baibulo lingathandize bwanji?

3 “Kodi Mwana Wangayu Watani?”

4 Polera Ana Luntha N’lofunika

6 Polera Ana Nzeru N’zofunika

12 Kumene Ndinamvera Dzina Loti Yehova

16 Kodi Akambuku Akuluakulu a ku Siberia Satheratu?

18 Zimene Achinyamata Amadzifunsa

Kodi Ndingatani Ngati Mbale Wanga Wadzipha?

21 Kodi Magazi Akayezedwa Ndiye Kuti Alibedi Kachilombo ka HIV?

22 Mitengo Yam’madzi

25 Chulu cha Chiswe

Chimapangidwadi Mwaluso

29 Kuchokera kwa Owerenga

30 Zochitika Padzikoli

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

32 Msonkhano wa Chigawo wa Mboni za Yehova Wakuti “Mzimu wa Mulungu Umatitsogolera”

Kodi Ndi Bwino Kumenyana ndi Wachiwembu? 10

Kodi munthu angatani ngati wakumana ndi wachiwembu? Kodi njira yabwino yodzitetezera ndi iti?

Zidole Zina si Zongoseweretsa 26

Atsikana ambiri ali ndi zidole zoseweretsa. Werengani nkhaniyi kuti mumve mbiri ya zidole komanso kuti muone kufunika kosamala nazo.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena